Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb21 March tsamba 2
  • Zimene Tingaphunzire pa Zomwe Zinkachitika pa Msasa wa Aisiraeli

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Zimene Tingaphunzire pa Zomwe Zinkachitika pa Msasa wa Aisiraeli
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
  • Nkhani Yofanana
  • Yehova Amatsogolera Anthu Ake
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
  • Yehova Anamenyera Nkhondo Aisiraeli
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
  • Muzikwaniritsa Zimene Mwalonjeza
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
  • Utumiki wa Alevi
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
Onani Zambiri
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
mwb21 March tsamba 2

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Zimene Tingaphunzire pa Zomwe Zinkachitika pa Msasa wa Aisiraeli

Amuna audindo amatsogolera pa utumiki wopatulika (Nu 7:10; it-1 497 ¶3)

Atumiki a Mulungu ayenera kuchita zinthu mwadongosolo (Nu 7:11; it-2 796 ¶1)

Yehova amadziwa kuti atumiki ake ena sangakwanitse kuchita zinthu zina (Nu 8:25, 26; w04 8/1 25 ¶1)

Mofanana ndi mmene ankachitira ndi Aisiraeli, masiku anonso Yehova amathandiza anthu ake kuchita zinthu mwadongosolo monga gulu. Komabe iye amaona mtumiki wake aliyense komanso khama limene amachita pomutumikira.

Amuna audindo akutsogolera pogwira ntchito za mpingo. 1. Mkulu ndi m’bale wachinyamata akupukuta mipando m’Nyumba ya Ufumu. 2. Mkulu akutsogolera kagulu komwe kakulalikira kunyumba ndi nyumba. 3. Mkulu akupemphera pa msonkhano wa akulu.
    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena