Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb21 March tsamba 4
  • N’chifukwa Chiyani Tiyenera Kupewa Mtima Wodandaula?

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • N’chifukwa Chiyani Tiyenera Kupewa Mtima Wodandaula?
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
  • Nkhani Yofanana
  • Chifukwa Chake Mkhalidwe Wamoyo wa Wodandaula Suli Wachimwemwe
    Nsanja ya Olonda—1993
  • Kodi Kudandaula Konse Nkoipa?
    Nsanja ya Olonda—1997
  • Yehova Amasintha Temberero N’kukhala Dalitso
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
  • Kodi Zochita za Munthu Mmodzi Zingasinthe Zinthu?
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
Onani Zambiri
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
mwb21 March tsamba 4
Mlongo amene wakhumudwa wapinda manja ndipo waima patali ndi anzake m’Nyumba ya Ufumu.

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

N’chifukwa Chiyani Tiyenera Kupewa Mtima Wodandaula?

Yehova sasangalala ndi mtima wodandaula (Nu 11:1; w01 6/15 17 ¶20)

Mtima wodandaula umasonyeza kuti munthu ndi wodzikonda komanso wosayamika (Nu 11:4-6; w06 7/15 15 ¶7)

Mtima wodandaula umafooketsa ena (Nu 11:10-15; it-2 719 ¶4)

Ngakhale kuti Aisiraeli ankakumana ndi mavuto ambiri m’chipululu, anali ndi zifukwa zambiri zoyamikira Yehova. Tingapewe mtima wodandaula ngati titamaganizira zinthu zambiri zimene Yehova watichitira.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena