Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb21 May tsamba 10
  • Malamulo a Yehova Amasonyeza Kuti Ndi Wanzeru Komanso Wachilungamo

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Malamulo a Yehova Amasonyeza Kuti Ndi Wanzeru Komanso Wachilungamo
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
  • Nkhani Yofanana
  • Mfundo Zothandiza Kuweruza Milandu Mwachilungamo
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
  • Mfumukazi Inaona Kuti Nzeru Ndi Zamtengo Wapatali
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
  • Kodi Chilamulo Chinkasonyeza Bwanji Kuti Yehova Amaganizira Anthu Osauka?
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
  • Tizitamanda Yehova Chifukwa ndi Wanzeru
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
Onani Zambiri
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
mwb21 May tsamba 10

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Malamulo a Yehova Amasonyeza Kuti Ndi Wanzeru Komanso Wachilungamo

Timasonyeza kuti ndife anzeru komanso ozindikira tikamamvera malamulo a Mulungu (De 4:6; it-2 1140 ¶5)

Anthu omwe amaona zochita zathu amazindikira kuti malamulo a Mulungu amatithandiza kukhala anzeru (De 4:6; w99 11/1 20 ¶6-7)

Anthu a Yehova amakhala moyo wosangalala kuposa anthu am’dzikoli (De 4:7, 8; w07 8/1 29 ¶13)

Anthu ambiri amabwera m’gulu la Yehova akaona makhalidwe abwino a anthu omwe amatsatira malamulo komanso mfundo za Mulungu pa moyo wawo.

M’bale yemwe akulalikira pogwiritsa ntchito kashelefu waona munthu wina yemwe wagwetsa waleti yake ndipo mzimayi amene ali pamalo odyera akuona zonsezo.
M’bale uja akupereka waletiyo kwa mwiniwake ndipo mzimayi uja akuona.

Kodi mwapeza madalitso otani chifukwa chotsatira malangizo anzeru ochokera kwa Yehova?

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena