Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb21 May tsamba 12
  • Phunzitsani Ana Anu Kuti Azikonda Yehova

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Phunzitsani Ana Anu Kuti Azikonda Yehova
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
  • Nkhani Yofanana
  • Muzikhala Ndi Mantha Oyenera Poopa Kukhumudwitsa Yehova
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
  • Kodi Makolo Angaphunzire Chiyani kwa Manowa ndi Mkazi Wake?
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
  • Zimene Adani Athu Amachita Pofuna Kutifooketsa
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
  • Malamulo a Yehova Amasonyeza Kuti Ndi Wanzeru Komanso Wachilungamo
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
Onani Zambiri
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
mwb21 May tsamba 12

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Phunzitsani Ana Anu Kuti Azikonda Yehova

Makolo ayenera kumakonda kwambiri Yehova (De 6:5; w05 6/15 20 ¶11)

Makolo ayenera kupereka chitsanzo chabwino kwa ana awo (De 6:6; w07 5/15 15-16)

Makolo ayenera kumaphunzitsa ana awo zokhudza Yehova nthawi zonse (De 6:7; w05 6/15 21 ¶14)

Kuwonjezera pa kulambira kwa pabanja, kodi ndi pa nthawi zinanso ziti pamene mungaphunzitse ana anu kuti azikonda Yehova komanso mfundo zake?

Bambo ndi mwana wake wamwamuna akupanga kayiti. Kumbuyo kwawo kuli magazini omwe akufotokoza zokhudza mbalame pa nkhani zakuti ‘Kodi Zinangochitika Zokha?’
Bambo akucheza ndi mwana wake wamkazi amene akuchekenira chithunzi cha mtengo wa maapozi. Bamboyo akuloza maapozi omwe ali m’mbale.
    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena