Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb23 March tsamba 10
  • Mfumukazi Inaona Kuti Nzeru Ndi Zamtengo Wapatali

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Mfumukazi Inaona Kuti Nzeru Ndi Zamtengo Wapatali
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
  • Nkhani Yofanana
  • Tizitamanda Yehova Chifukwa ndi Wanzeru
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
  • Ulendo Umene Unali Wopindulitsa Kwambiri
    Nsanja ya Olonda—1999
  • Malamulo a Yehova Amasonyeza Kuti Ndi Wanzeru Komanso Wachilungamo
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
  • Solomo Anapemphera Modzichepetsa Komanso Mochokera Pansi pa Mtima
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
mwb23 March tsamba 10
Mfumukazi ya ku Sheba yabweretsa mphatso kwa Mfumu Solomo. Iye waimirira kuti alandire mfumukaziyo. Oimba ndi alonda aima mmunsi mwa masitepe opita ku mpando wachifumu wa Solomo.

Mfumukazi ya ku Sheba yakacheza kwa Mfumu Solomo

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Mfumukazi Inaona Kuti Nzeru Ndi Zamtengo Wapatali

Mfumukazi ya ku Sheba inayenda ulendo wautali komanso wovuta kuti ikaone Solomo (2Mb 9:1, 2; w99 11/1 20 ¶4; w99 7/1 30 ¶4-5)

Nzeru komanso chuma cha Solomo zinamusowetsa chonena (2Mb 9:3, 4; w99 7/1 30-31; onani chithunzi chapachikuto)

Zimene anaona zinamuchititsa kuti atamande Yehova (2Mb 9:7, 8; it-2 990-991)

Mfumukazi ya ku Sheba yakwera pa ngamila kukakumana ndi Mfumu Solomo.

Mfumukazi ya ku Sheba inaona kuti nzeru ndi zamtengo wapatali moti inachita zonse zomwe ikanatha kuti ikhale nazo.

DZIFUNSENI KUTI, ‘Kodi ndine wofunitsitsa kufunafuna nzeru ngati mmene ndingachitire ndi chuma chobisika?’​—Miy 2:1-6.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena