Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb22 September tsamba 2
  • Tizitamanda Yehova Chifukwa ndi Wanzeru

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Tizitamanda Yehova Chifukwa ndi Wanzeru
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
  • Nkhani Yofanana
  • Mfumukazi Inaona Kuti Nzeru Ndi Zamtengo Wapatali
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
  • Ulendo Umene Unali Wopindulitsa Kwambiri
    Nsanja ya Olonda—1999
  • Solomo Anapemphera Modzichepetsa Komanso Mochokera Pansi pa Mtima
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
  • Nzeru Ndi Zamtengo Wapatali
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
Onani Zambiri
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
mwb22 September tsamba 2

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Tizitamanda Yehova Chifukwa ndi Wanzeru

Yehova anapatsa Solomo nzeru zapadera (1Mf 10:1-3; w99 7/1 30 ¶6)

Mfumukazi ya ku Sheba inachita chidwi ndi nzeru zimene Yehova anapatsa Solomo (1Mf 10:4, 5; w99 11/1 20 ¶6)

Mfumukazi ya ku Sheba inatamanda Yehova chifukwa chosankha Solomo kuti akhale mfumu (1Mf 10:6-9; w99 7/1 30-31)

Mlongo akulalikira mzimayi pa malo odyera.

Mofanana ndi mfumukazi ya ku Sheba, nafenso tingasonyeze kuti timayamikira nzeru zimene Mulungu anatipatsa. Njira imodzi ndi kugwiritsa ntchito zimene Yesu anaphunzitsa komanso kuchita zonse zomwe tingathe kuti titengere chitsanzo chake. (Mt 12:42; 1Pe 2:21) Njira inanso ndi kuuza ena nzeru za Mulungu tikakhala mu utumiki.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena