Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb21 July tsamba 8
  • Kodi Chilamulo Chinkasonyeza Bwanji Kuti Yehova Amaganizira Zinyama?

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Kodi Chilamulo Chinkasonyeza Bwanji Kuti Yehova Amaganizira Zinyama?
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
  • Nkhani Yofanana
  • Yehova Anachita Zinthu Mwanzeru Pogawa Malo
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
  • Nyama
    Galamukani!—2015
  • Yehova Anamenyera Nkhondo Aisiraeli
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
  • Kodi Yehova Amafuna Kuti Tizimulambira Bwanji?
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
Onani Zambiri
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
mwb21 July tsamba 8

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Kodi Chilamulo Chinkasonyeza Bwanji Kuti Yehova Amaganizira Zinyama?

Nyama imene yakumana ndi vuto linalake inkafunika kuthandizidwa (De 22:4; it-1 375-​376)

Mbalame yaikazi yomwe ili ndi ana kapena mazira sinkafunika kuchitidwa nkhanza (De 22:​6, 7; it-1 621 ¶1)

Nyama zosiyana sizinkayenera kumangidwa pa goli limodzi (De 22:10; w03 10/15 32 ¶1-2)

Ng’ombe ndi bulu zamangidwa pa goli limodzi. Golilo lapendekeka chifukwa nyamazi ndi zosiyana misinkhu.

Yehova amakhudzidwa ndi mmene timachitira zinthu ndi nyama. Sitiyenera kuchitira nkhanza zinyama kapena kuzipha pongofuna kusangalala.​—Miy 12:10.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena