Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb22 January tsamba 3
  • Kusamvera Malamulo a Mulungu Kumabweretsa Mavuto

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Kusamvera Malamulo a Mulungu Kumabweretsa Mavuto
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
  • Nkhani Yofanana
  • Yefita Anali Munthu Wauzimu
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
  • Kodi Chilamulo Chinkasonyeza Bwanji Kuti Yehova Amaganizira Anthu Osauka?
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
  • Tidzayenda M’dzina la Yehova Mpaka Muyaya!
    Nsanja ya Olonda—2003
  • Atumiki a Yehova Ali ndi Chiyembekezo Chenicheni
    Nsanja ya Olonda—2003
Onani Zambiri
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
mwb22 January tsamba 3

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Kusamvera Malamulo a Mulungu Kumabweretsa Mavuto

Mika anawabera mayi ake ndalama (Owe 17:1, 2)

Mika ankalambira mafano komanso sanatsatire dongosolo la Yehova lokhudza chihema ndi unsembe (Owe 17:4, 5, 12; it-2 390-391)

Pamapeto pake Mika anatsala wopanda kanthu (Owe 18:24-26; it-2 391 ¶2)

Mayi amene kale anali wa Mboni, ndipo panopa ali ndi mwana, akuganizira mmene ankasangalalira pa nthawi imene ankatumikira Yehova. Patebulo pali kambale koikamo phulusa la ndudu momwe muli zidutswa za ndudu. Bambo waledzera ndipo wagona pampando.

DZIFUNSENI KUTI, ‘Kodi kumvera Yehova kwandithandiza bwanji?’

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena