Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb22 January tsamba 6
  • Muzisonyeza Chikondi Chokhulupirika

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Muzisonyeza Chikondi Chokhulupirika
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
  • Nkhani Yofanana
  • Pitirizani Kusonyezana Chikondi Chokhulupirika
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2021
  • “Kumene Inu Mupite Inenso Ndipita Komweko”
    Tsanzirani Chikhulupiriro Chawo
  • “Kumene Inu Mupite Inenso Ndipita Komweko”
    Nsanja ya Olonda—2012
  • Rute ndi Naomi
    Zimene Tingaphunzire Munkhani za M’Baibulo
Onani Zambiri
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
mwb22 January tsamba 6

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Muzisonyeza Chikondi Chokhulupirika

[Onerani vidiyo yakuti Mfundo Zothandiza Kumvetsa Buku la Rute.]

Naomi anauza Olipa ndi Rute kuti abwerere ku Mowabu (Ru 1:8-13; w16.02 14 ¶5)

Rute anakana kusiya Naomi komanso Yehova (Ru 1:16, 17; w16.02 14 ¶6)

Zithunzi: 1. Amayi ndi mwana wawo akucheza ndi banja kudzera pa intaneti. 2. Banja lija latenga chakudya chophikaphika komanso basiketi momwe muli zakudya zina kupita nazo kwa amayi aja ndi mwana wawo.

Timasonyeza ena chikondi chokhulupirika ngati tili odzipereka, okhulupirika komanso ngati tili nawo pa ubwenzi wabwino. Yehova amasonyeza chikondi chokhulupirika kwa atumiki ake okhulupirika. (Sl 63:3) Ifenso tizisonyeza chikondi chokhulupirika kwa anthu ena.​—Miy 21:21.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena