Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb22 January tsamba 12
  • Yehova Amatiganizira

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Yehova Amatiganizira
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
  • Nkhani Yofanana
  • Kodi Mukukumbukira?
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2018
  • Tizidzichepetsa Zinthu Zikatiyendera
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
  • Zimene Tingaphunzire kwa Samueli
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
  • “Ndinamutsutsa Pamasom’pamaso”
    Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2019
Onani Zambiri
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
mwb22 January tsamba 12
Zithunzi: 1. Samueli ali mwana akumvetsera pamene Yehova akumulankhula. 2. Samueli akuuza Eli uthenga wochokera kwa Yehova.

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Yehova Amatiganizira

Samueli ankaganiza kuti Eli akumuitana (1Sa 3:4-7; w18.09 24 ¶3)

Yehova anatsimikizira Samueli kuti iyeyo ndi amene amamuitana (1Sa 3:8, 9)

Yehova anasonyeza kuti ankaganizira Samueli yemwe anali wamng’ono (1Sa 3:15-18; w18.09 24 ¶4)

DZIFUNSENI KUTI: ‘Kodi ndingasonyeze bwanji kuti ndimaganizira achinyamata komanso achikulire? Kodi ndingasonyeze bwanji kuti ndimaganizira ena ndikakhala kumisonkhano ya Chikhristu?’

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena