Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb22 March tsamba 6
  • Tizidzichepetsa Zinthu Zikatiyendera

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Tizidzichepetsa Zinthu Zikatiyendera
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
  • Nkhani Yofanana
  • Tiziyembekezera Yehova Moleza Mtima
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
  • Yehova Amatiganizira
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
  • Kumvera Kumaposa Nsembe
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
  • Mmene Davide Ankamenyera Nkhondo
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
Onani Zambiri
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
mwb22 March tsamba 6

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Tizidzichepetsa Zinthu Zikatiyendera

Aisiraeli anatamanda Davide (1Sa 18:5-7; w04 4/1 15 ¶4)

Yehova ankathandiza Davide kuti zinthu zimuyendere bwino (1Sa 18:14)

Davide anapitiriza kukhala wodzichepetsa (1Sa 18:22, 23; w18.01 28 ¶6-7)

Zithunzi: 1. M’bale akukamba nkhani pa msonkhano. 2. Anthu ena akuyamikira m’bale uja komanso kuchita naye chidwi, koma iye modzichepetsa akukana kutamandidwa.

N’chifukwa chiyani tiyenera kukhalabe odzichepetsa Yehova akamatidalitsa? Kodi n’chiyani chingatithandize kuti tikhalebe odzichepetsa?

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena