Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb22 May tsamba 2
  • Mmene Davide Ankamenyera Nkhondo

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Mmene Davide Ankamenyera Nkhondo
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
  • Nkhani Yofanana
  • Kumvera Kumaposa Nsembe
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
  • Tiziyembekezera Yehova Moleza Mtima
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
  • Tizidzichepetsa Zinthu Zikatiyendera
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
  • Kodi Ndi pa Nthawi Iti Pamene Tiyenera Kudalira Yehova?
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
Onani Zambiri
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
mwb22 May tsamba 2

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Mmene Davide Ankamenyera Nkhondo

Davide ankafuna kuthawa Sauli (1Sa 27:5-7; it-1 41)

Davide anateteza malire a Yuda (1Sa 27:8, 9; w21.03 4 ¶8)

Davide sanauze Akisi zonse zimene ankachita (1Sa 27:10-12; it-2 245 ¶6)

M’bale wakhala chete pamene apolisi akumufunsa mafunso.

Masiku ano akuluakulu a boma akhoza kuletsa ntchito yathu ya Ufumu komanso akhoza kutifunsa zokhudza abale athu. Pa nthawi ngati imeneyi ndi bwino kukhala chete kuti tisaike abale athu pangozi.—Miy 10:19; 11:12; Mla 3:7.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena