CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
Kumvera Kumaposa Nsembe
Mneneri wa Yehova anapereka malangizo omveka bwino kwa Mfumu Sauli (1Sa 15:3)
Sauli anapereka zifukwa zodzikhululukira chifukwa sanamvere zonse zimene Yehova anamuuza (1Sa 15:13-15)
Yehova savomereza kulambira kwa anthu omwe samumvera (1Sa 15:22, 23; w07 6/15 26 ¶4; it-2 521 ¶2)
DZIFUNSENI KUTI, ‘Kodi ndimamvera malangizo ochokera ku gulu la Yehova mwamsanga komanso ndi mtima wonse?’