Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb22 March tsamba 2
  • Kudzikuza Kumabweretsa Manyazi

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Kudzikuza Kumabweretsa Manyazi
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
  • Nkhani Yofanana
  • Kumvera Kumaposa Nsembe
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
  • Sauli Anali Wodzichepetsa Poyamba
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
  • Kudzikuza Kumadzetsa Manyazi
    Nsanja ya Olonda—2000
  • “Kumvera Kuposa Nsembe”
    Nsanja ya Olonda—2011
Onani Zambiri
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
mwb22 March tsamba 2
Mfumu Sauli anachita zinthu modzikuza popereka nsembe yopsereza pa guwa.

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Kudzikuza Kumabweretsa Manyazi

Mfumu Sauli inkamva kuti yapanikizika (1Sa 13:5-7)

Sauli anachita zinthu modzikuza m’malo motsatira malangizo a Yehova modzichepetsa (1Sa 13:8, 9; w00 8/1 13 ¶17)

Yehova anadzudzula Sauli (1Sa 13:13, 14; w07 6/15 27 ¶8)

Munthu amasonyeza kuti ndi wodzikuza akachita zinthu zomwe si udindo wake mopupuluma kapena mopusa. Kudzikuza n’kosiyana ndi kudzichepetsa. Kodi ndi pazochitika ziti pamene munthu angayesedwe kuti achite zinthu modzikuza?

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena