Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb22 March tsamba 10-11
  • Ndandanda Yowerengera Baibulo pa Nyengo ya Chikumbutso cha 2022

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Ndandanda Yowerengera Baibulo pa Nyengo ya Chikumbutso cha 2022
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
  • Timitu
  • Nkhani Yofanana
  • Loweruka, 9 April
  • Lamlungu, 10 April
  • Lolemba, 11 April
  • Lachiwiri, 12 April
  • Lachitatu, 13 April
  • Lachinayi, 14 April
  • Lachisanu, 15 April
  • Tsiku la Chikumbutso (Dzuwa Litalowa)
  • Loweruka, 16 April
  • Lamlungu, 17 April
  • Lolemba, 18 April
  • Ndandanda Yowerengera Baibulo pa Nyengo ya Chikumbutso cha 2025
    Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Kabuku ka Msonkhano—2025
  • Ndandanda Yowerengera Baibulo pa Nyengo ya Chikumbutso cha 2023
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
  • Ndandanda Yowerengera Baibulo pa Nyengo ya Chikumbutso cha 2024
    Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Kabuku ka Msonkhano—2024
  • B12-B Wiki Yomaliza ya Moyo wa Yesu Padziko Lapansi (Gawo 2)
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
Onani Zambiri
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
mwb22 March tsamba 10-11

Ndandanda Yowerengera Baibulo pa Nyengo ya Chikumbutso cha 2022

Loweruka, 9 April

M’MAWA

MADZULO (Kuyamba kwa Nisani 8)

  • Yohane 11:55–12:11

Lamlungu, 10 April

Yesu watsamira tebulo ndipo Mariya akumuthira mafuta onunkhira pamutu.

M’MAWA

MADZULO (Kuyamba kwa Nisani 9)

  • Mateyu 26:6-13

  • Maliko 14:3-9

  • Yohane 12:2-11

Yesu​—Ndi Njira, mutu 101

Lolemba, 11 April

Yesu wakwera bulu. Anthu akuika malaya awo akunja komanso nthambi za kanjedza mumsewu.

M’MAWA

  • Mateyu 21:1-11, 14-17

  • Maliko 11:1-11

  • Luka 19:29-44

  • Yohane 12:12-19

Yesu​—Ndi Njira, mutu 102

MADZULO (Kuyamba kwa Nisani 10)

Lachiwiri, 12 April

Yesu akugubuduza matebulo a anthu osintha ndalama pakachisi.

M’MAWA

  • Mateyu 21:12, 13, 18, 19

  • Maliko 11:12-19

  • Luka 19:45-48

  • Yohane 12:20-50

Yesu​—Ndi Njira, mutu 103-104

MADZULO (Kuyamba kwa Nisani 11)

Lachitatu, 13 April

Yesu ndi atumwi ake akuona mkazi wamasiye wosauka akuponya timakobidi tiwiri tating’ono moponyamo zopereka.

M’MAWA

  • Mateyu 21:19–25:46

  • Maliko 11:20–13:37

  • Luka 20:1–21:38

Yesu​—Ndi Njira, mutu 105-114

MADZULO (Kuyamba kwa Nisani 12)

Lachinayi, 14 April

Yudasi Isikariyoti akukonza chiwembu ndi atsogoleri a chipembedzo.

M’MAWA

  • Mateyu 26:1-5, 14-16

  • Maliko 14:1, 2, 10, 11

  • Luka 22:1-6

Yesu​—Ndi Njira, mutu 115

MADZULO (Kuyamba kwa Nisani 13)

Lachisanu, 15 April

Tsiku la Chikumbutso (Dzuwa Litalowa)

Yesu ndi atumwi ake okhulupirika ali patebulo pa nthawi ya Chakudya Chamadzulo cha Ambuye.

M’MAWA

  • Mateyu 26:17-19

  • Maliko 14:12-16

  • Luka 22:7-13

MADZULO (Kuyamba kwa Nisani 14)

  • Mateyu 26:20-75

  • Maliko 14:17-72

  • Luka 22:14-65

  • Yohane 13:1–18:27

Yesu​—Ndi Njira, mutu 116-126

Loweruka, 16 April

Yesu wapachikidwa pamtengo wozunzikirapo limodzi ndi chigawenga.

M’MAWA

  • Mateyu 27:1-61

  • Maliko 15:1-47

  • Luka 22:66–23:56

  • Yohane 18:28–19:42

Yesu​—Ndi Njira, mutu 127-133

MADZULO (Kuyamba kwa Nisani 15)

Lamlungu, 17 April

Atsogoleri a chipembedzo akulankhula ndi Pilato.

M’MAWA

  • Mateyu 27:62-66

MADZULO (Kuyamba kwa Nisani 16)

  • Maliko 16:1

Lolemba, 18 April

Akazi akudabwa kuona kuti Yesu mulibe m’manda amene anaikidwamo.

M’MAWA

  • Mateyu 28:1-15

  • Maliko 16:2-8

  • Luka 24:1-49

  • Yohane 20:1-25

Yesu​—Ndi Njira, mutu 134-135

MADZULO (Kuyamba kwa Nisani 17)

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena