Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb23 March tsamba 8-9
  • Ndandanda Yowerengera Baibulo pa Nyengo ya Chikumbutso cha 2023

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Ndandanda Yowerengera Baibulo pa Nyengo ya Chikumbutso cha 2023
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
  • Timitu
  • Nkhani Yofanana
  • LACHITATU, 29 MARCH
  • LACHINAYI, 30 MARCH
  • LACHISANU, 31 MARCH
  • LOWERUKA, 1 APRIL
  • LAMLUNGU, 2 APRIL
  • LOLEMBA, 3 APRIL
  • LACHIWIRI, 4 APRIL
  • TSIKU LA CHIKUMBUTSO (DZUWA LITALOWA)
  • LACHITATU, 5 APRIL
  • LACHINAYI, 6 APRIL
  • LACHISANU, 7 APRIL
  • Ndandanda Yowerengera Baibulo pa Nyengo ya Chikumbutso cha 2022
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
  • Ndandanda Yowerengera Baibulo pa Nyengo ya Chikumbutso cha 2025
    Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Kabuku ka Msonkhano—2025
  • Ndandanda Yowerengera Baibulo pa Nyengo ya Chikumbutso cha 2024
    Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Kabuku ka Msonkhano—2024
  • B12-B Wiki Yomaliza ya Moyo wa Yesu Padziko Lapansi (Gawo 2)
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
mwb23 March tsamba 8-9
Yesu wanyamula mtengo wake wozunzikirapo.

Ndandanda Yowerengera Baibulo Pa Nyengo Ya Chikumbutso Cha 2023

LACHITATU, 29 MARCH

M’MAWA

MADZULO (Kuyamba kwa Nisani 8)

LACHINAYI, 30 MARCH

Mariya akuthira mafuta onunkhira pamutu pa Yesu pamene iye wakhala motsamira tebulo.

M’MAWA

MADZULO (Kuyamba kwa Nisani 9)

Yesu​—Ndi Njira, mutu 101

LACHISANU, 31 MARCH

Yesu wakwera mwana wa bulu pamene anthu ambiri akusangalala ndipo ena akuyala zovala zawo zakunja komanso nthambi za kanjedza mumsewu.

M’MAWA

Yesu​—Ndi Njira, mutu 102

MADZULO (Kuyamba kwa Nisani 10)

LOWERUKA, 1 APRIL

Yesu akugubuduza matebulo a osintha ndalama m’kachisi.

M’MAWA

Yesu​—Ndi Njira, mutu 103-104

MADZULO (Kuyamba kwa Nisani 11)

LAMLUNGU, 2 APRIL

Yesu ndi atumwi ake akuyang’ana mwachidwi mayi wamasiye amene akuponya tindalama tiwiri moponyamo ndalama m’kachisi.

M’MAWA

Yesu​—Ndi Njira, mutu 105-114

MADZULO (Kuyamba kwa Nisani 12)

LOLEMBA, 3 APRIL

Yudasi Isikarioti akukonza chiwembu ndi atsogoleri a chipembedzo. Ndalama za siliva zikuonekera.

M’MAWA

Yesu​—Ndi Njira, mutu 115

MADZULO (Kuyamba kwa Nisani 13)

LACHIWIRI, 4 APRIL

TSIKU LA CHIKUMBUTSO (DZUWA LITALOWA)

Yesu ndi atumwi ake akhala mozungulira pa tebulo pa nthawi ya Chakudya Chamadzulo cha Ambuye.

M’MAWA

MADZULO (Kuyamba kwa Nisani 14)

Yesu​—Ndi Njira, mutu 116-126

LACHITATU, 5 APRIL

Yesu wapachikidwa pa mtengo wozunzikirapo limodzi ndi chigawenga.

M’MAWA

Yesu​—Ndi Njira, mutu 127-133

MADZULO (Kuyamba kwa Nisani 15)

LACHINAYI, 6 APRIL

Atsogoleri achipembedzo akupempha Pontiyo Pilato.

M’MAWA

MADZULO (Kuyamba kwa Nisani 16)

LACHISANU, 7 APRIL

Azimayi atatu akusunzumira m’manda omwe munaikidwa Yesu.

M’MAWA

Yesu​—Ndi Njira, mutu 134-135

MADZULO (Kuyamba kwa Nisani 17)

Mapu osonyeza Yerusalemu ndi mizinda yozungulira. Malo amene ankadziwika bwino ndi awa. 1. Kachisi. 2. Munda wa Getsemane. 3. Nyumba ya Bwanamkubwa. 4. Nyumba ya Kayafa. 5. Nyumba Imene Herode Antipa Ankakhala. 6. Dziwe la Betesida. 7. Dziwe la Siloamu. 8. Holo ya Khoti Lalikulu la Ayuda. 9. Gologota. 10. Munda wa Magazi.
    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena