Ndandanda Yowerengera Baibulo pa Nyengo ya Chikumbutso ya 2026
Malifalensi amene ali pansiwa akufotokoza zinthu zofunika zimene zinachitika zaka 1,993 zapitazo, pa tsiku lofanana ndi limene lasonyezedwa. Mungasankhe kuchuluka kwa zimene mukufuna kuwerenga tsiku lililonse.
LACHISANU, MARCH 27
DZUWA LITATULUKA
DZUWA LITALOWA (Kuyamba kwa Nisani 8)
LOWERUKA, MARCH 28
LAMLUNGU, MARCH 29
LOLEMBA, MARCH 30
LACHIWIRI, MARCH 31
LACHITATU, APRIL 1
LACHINAYI, APRIL 2
TSIKU LA CHIKUMBUTSO (DZUWA LITALOWA)