Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb22 March tsamba 16
  • Zimene Tinganene

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Zimene Tinganene
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
  • Timitu
  • Nkhani Yofanana
  • Ntchito Yoitanira Anthu ku Chikumbutso (19 March–15 April)
  • Ulendo Woyambaa (March 1-18, April 16-30)
  • Ulendo Wobwerezab
  • Zimene Tinganene
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
  • Zimene Tinganene
    Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2019
  • Zimene Tinganene
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
  • Zimene Tinganene
    Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
Onani Zambiri
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
mwb22 March tsamba 16
Mwamuna ndi mkazi wake akulandira anthu mwansangala panja pa Nyumba ya Ufumu.

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

Zimene Tinganene

Ntchito Yoitanira Anthu ku Chikumbutso (19 March–15 April)

“Ndife osangalala kukuitanirani kumwambo wofunika kwambiri womwe udzachitike padziko lonse. Mwambo umenewu ndi wokumbukira imfa ya Yesu.” M’patseni kapepala kosindikizidwa kapena ka pachipangizo chamakono. “Kapepalaka kakusonyeza nthawi komanso malo omwe mwambowu udzachitikire m’dera lathu lino [kapena zimene mungachite kuti muchite nawo mwambowu pa intaneti]. Tikukuitananinso kuti mudzamvetsere nkhani yapadera yomwe idzakambidwe kumapeto kwa mlungu woyambira April 4.”

Ngati Munthuyo Wasonyeza Chidwi: Musonyezeni [kapena mutumizireni linki ya] vidiyo yakuti Tizikumbukira Imfa ya Yesu.

Funso la Ulendo Wotsatira: N’chifukwa chiyani Yesu anafa?

Ulendo Woyambaa (March 1-18, April 16-30)

Funso: Kodi Yesu ndi ndani?

Lemba: Mt 16:16

Funso la Ulendo Wotsatira: N’chifukwa chiyani Yesu anafa?

Ulendo Wobwerezab

Funso: N’chifukwa chiyani Yesu anafa?

Lemba: Mt 20:28

Funso la Ulendo Wotsatira: Kodi tingasonyeze bwanji kuti timayamikira nsembe ya dipo ya Yesu?

a b Mukhoza kusintha mafunsowa komanso zimene zikuchitika kuti zigwirizane ndi mmene zinthu zilili kwanuko.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena