Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb22 May tsamba 8
  • Yehova Anachita Pangano ndi Davide

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Yehova Anachita Pangano ndi Davide
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
  • Nkhani Yofanana
  • Muzidalira Yehova Kuti Akuthandizeni
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
  • ‘Madalitso Onsewa . . . Adzakupeza’
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
  • Zimene Yobu Anachita Kuti Akhalebe Woyera
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
  • Musamaone Zinthu Zopanda Pake
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
Onani Zambiri
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
mwb22 May tsamba 8
Mfumu Davide ili pawindo la nyumba yachifumu, ndipo ikuyang’ana panja.

Davide akuganizira mozama za pangano limene Yehova anapangana naye

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Yehova Anachita Pangano ndi Davide

Yehova analonjeza Davide kuti adzakhazikitsa ufumu m’banja lake (2Sa 7:11, 12; w10 4/1 20 ¶3; onani chithunzi chapachikuto)

Mbali zina za pangano limene Yehova anachita ndi Davide zinakwaniritsidwa pa Mesiya (2Sa 7:13, 14; Ahe 1:5; w10 4/1 20 ¶4)

Zinthu zabwino zimene zinabwera chifukwa cha ulamuliro wa Mesiya zidzakhalapo mpaka kalekale (2Sa 7:15, 16; Ahe 1:8; w14 10/15 10 ¶14)

Yesu ali kumwamba pampando wachifumu ndipo akuyang’ana dziko lapansi.

Dzuwa ndi mwezi zimatikumbutsa kuti ulamuliro wa Mesiya udzakhalapo mpaka kalekale. (Sl 89:35-37) Mukamaona zinthu zimenezi muziganizira madalitso amene Yehova anakulonjezani inuyo komanso anthu a m’banja lanu kudzera mu Ufumu wake.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena