Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb22 July tsamba 6
  • Muzidalira Yehova Kuti Akuthandizeni

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Muzidalira Yehova Kuti Akuthandizeni
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
  • Nkhani Yofanana
  • Yehova Anachita Pangano ndi Davide
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
  • Yehova ndi Mulungu Wachilungamo
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
  • Kodi Mumapereka Nsembe?
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
  • Kudzikonda kwa Aminoni Kunabweretsa Mavuto
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
Onani Zambiri
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
mwb22 July tsamba 6

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Muzidalira Yehova Kuti Akuthandizeni

Yehova amamva tikamamupempha thandizo (2Sa 22:7)

Yehova ndi wamphamvu kuposa mdani aliyense (2Sa 22:14-18; cl 19 ¶11)

Yehova amachita zinthu mokhulupirika ndipo amatithandiza (2Sa 22:26; w10 6/1 26 ¶4-6)

Zithunzi: 1. Mlongo wachitsikana wakhala pansi pamene amayi ake akumulalatira komanso kumung’ambira mabuku. 2. Mlongo yemwe uja akuwerenga Baibulo. 3. Akucheza ndi abale ndi alongo ku Nyumba ya Ufumu.

Yehova ali ndi mphamvu yochotsa mavuto athu onse. Komabe, nthawi zambiri amatithandiza kupirira pogwiritsa ntchito mzimu wake woyera, Mawu ake komanso abale athu a Chikhristu. (Sl 55:22) Kodi tingatani kuti Mulungu azitithandiza?

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena