Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb22 July tsamba 7
  • Kodi Mumapereka Nsembe?

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Kodi Mumapereka Nsembe?
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
  • Nkhani Yofanana
  • Kodi Tikuphunzira Chiyani Kuchokera pa Nyimbo Yotchedwa “Uta”?
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
  • Abisalomu Anaukira Chifukwa cha Kunyada
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
  • Yehova ndi Mulungu Wachilungamo
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
  • Kudzikonda kwa Aminoni Kunabweretsa Mavuto
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
Onani Zambiri
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
mwb22 July tsamba 7

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Kodi Mumapereka Nsembe?

Davide anauzidwa kuti amange guwa la nsembe pamalo opunthira mbewu a Arauna (2Sa 24:18)

Arauna ananena kuti apereka malo komanso nyama zoti apereke nsembe (2Sa 24:21-23)

Davide sakanapereka nsembe popanda kulipira (2Sa 24:24, 25; it-1 146)

Zithunzi zosonyeza njira zimene tingaperekere nsembe: 1. Abale ndi alongo akuthandiza pa ntchito yomanga Nyumba ya Ufumu. 2. Mlongo wachikulire akuponya ndalama m’bokosi la zopereka. 3. Banja likulalikira pogwiritsa ntchito kashelefu. 4. Abale ndi alongo akuthandiza anthu amene akhudzidwa ndi ngozi zadzidzidzi.

Yehova amasangalala tikamapereka nthawi yathu, mphamvu zathu komanso zinthu zathu ndi mtima wonse kuti zinthu za Ufumu ziziyenda bwino. (w12 1/15 18 ¶8) Kodi mungakhale ndi zolinga zotani kuti muwonjezere ‘nsembe zimene mumapereka potamanda’ Mulungu?​—Ahe 13:15.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena