Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb22 July tsamba 12
  • Kodi Tikuphunzira Chiyani pa Zipilala Ziwiri?

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Kodi Tikuphunzira Chiyani pa Zipilala Ziwiri?
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
  • Nkhani Yofanana
  • B8 Kachisi Amene Solomo Anamanga
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
  • Anagwira Ntchito Mwamphamvu Komanso ndi Mtima Wonse
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
  • Zimene Mungachite Kuti Zinthu Zizikuyenderani Bwino
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
  • Muzilimbikitsa Abale ndi Alongo Anu Akakumana ndi Mavuto
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
mwb22 July tsamba 12
Zipilala ziwiri zamkuwa zomwe zili m’mbali mwa khonde la kachisi.

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Kodi Tikuphunzira Chiyani pa Zipilala Ziwiri?

Zipilala ziwiri zikuluzikulu zinamangidwa moonekera bwino pakhonde la kachisi (1Mf 7:15, 16; w13 12/1 13 ¶3)

Zipilalazi anazipatsa mayina atanthauzo; Yakini lomwe limatanthauza kuti “Yehova Akhazikitse” komanso Boazi lomwe n’kutheka limatanthauza kuti “Mu Mphamvu” (1Mf 7:21; it-1 348)

Yehova akanathandiza anthu ake kumanga kachisi molimba ngati iwo akanamamudalira (Sl 127:1)

Yehova anatithandiza kulimbana ndi mavuto ambirimbiri kuti tiphunzire choonadi. Koma tiyenera kupitiriza kumudalira kuti tikhalebe ‘olimba m’chikhulupiriro.’​—1Ak 16:13.

Zithunzi: 1. Mtsikana akugula zinthu ndipo walandira kabuku kakuti “Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale” kuchokera kwa mlongo. 2. Mtsikana uja akuganizira za khalidwe lake losuta fodya pamene akuwerenga buku lakuti “Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale” ali kunyumba kwake. 3. Akubatizidwa.

DZIFUNSENI KUTI, ‘Kodi ndimasonyeza bwanji kuti ndimadalira Yehova?’

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena