KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Zimene Tinganene
Ulendo Woyamba
Funso: N’chifukwa chiyani Mulungu analenga anthu?
Lemba: Ge 1:28
Funso la Ulendo Wotsatira: Kodi timadziwa bwanji kuti cholinga cha Mulungu polenga anthu chidzakwaniritsidwa?
Ulendo Wobwereza
Funso: Kodi timadziwa bwanji kuti cholinga cha Mulungu polenga anthu chidzakwaniritsidwa?
Lemba: Yes 55:11
Funso la Ulendo Wotsatira: Kodi moyo udzakhala wotani Mulungu akadzakwaniritsa cholinga chimene analengera anthu?