Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb22 September tsamba 4
  • Sankhani Mwanzeru Munthu Wokwatirana Naye

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Sankhani Mwanzeru Munthu Wokwatirana Naye
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
  • Nkhani Yofanana
  • Kodi Mukukumbukira?
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2018
  • Muzithandiza Achinyamata Kuti Azichita Zambiri
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
  • Yehova Amatiganizira
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
  • “Ndinamutsutsa Pamasom’pamaso”
    Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2019
Onani Zambiri
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
mwb22 September tsamba 4

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Sankhani Mwanzeru Munthu Wokwatirana Naye

Solomo anachita zinthu mopanda nzeru pokwatira akazi amene ankalambira milungu yonyenga (1Mf 11:1, 2; w18.07 18 ¶7)

Pang’ono ndi pang’ono, akazi a Solomo anamuchititsa kuti asiye kulambira Yehova (1Mf 11:3-6; w19.01 15 ¶6)

Yehova anakwiyira kwambiri Solomo (1Mf 11:9, 10; w18.07 19 ¶9)

Zithunzi: Mlongo wosakwatiwa akuphunzira Baibulo payekha ndipo akuganizira m’bale wosakwatira. 1. M’bale akupereka ndemanga pamisonkhano ya mpingo. 2. Akulalikira pa malo opezeka anthu ambiri. 3. Akuthandiza nawo kukonza Nyumba ya Ufumu.

Mawu a Mulungu amalimbikitsa Akhristu amene akufuna kulowa m’banja kuti, akwatire kapena akwatiwe “mwa Ambuye.” (1Ak 7:39) Komabe, kubatizidwa pakokha sikungapangitse munthu kukhala woyenera. Kodi munthu amene mukufuna kukwatirana nayeyo, adzakuthandizani kutumikira Yehova ndi mtima wonse? Kodi wasonyeza kuti amakonda Yehova kwa nthawi ndithu? Musanatsimikize zokwatirana ndi munthu winawake, muzikhala ndi nthawi yokwanira kuti mumudziwe bwino.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena