Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb23 January tsamba 14
  • Muzithandiza Achinyamata Kuti Azichita Zambiri

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Muzithandiza Achinyamata Kuti Azichita Zambiri
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
  • Nkhani Yofanana
  • Yesetsani Kukhala Odzichepetsa Ngati Esitere
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
  • Kodi Mukukumbukira?
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2018
  • “Nyamulani Mwana Wanu”
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
  • Malangizo Achikondi a Bambo Opita kwa Mwana Wake
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
mwb23 January tsamba 14
Mfumu Davide akusonyeza Solomo amuna ogwira ntchito amene akukonza zinthu zodzamangira kachisi.

Chithunzi chapachikuto: Davide akupereka anthu ogwira ntchito komanso zipangizo zomangira kachisi kwa Solomo

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Muzithandiza Achinyamata Kuti Azichita Zambiri

Davide ankadziwa kuti mothandizidwa ndi Yehova, Solomo adzakwanitsa kuyang’anira ntchito yonse yomanga kachisi (1Mb 22:5; w17.01 29 ¶8)

Davide analimbikitsa Solomo kuti azidalira Yehova n’kumachita zoyenera (1Mb 22:11-13)

Davide anali wofunitsitsa kuthandiza Solomo (1Mb 22:14-16; w17.01 29 ¶7; onani chithunzi chapachikuto)

Zithunzi: 1. Mkulu akuphunzitsa m’bale wachinyamata zokhudza mmene angasamalire gawo la mpingo wawo. Iye akumusonyeza mapu a gawo la mpingo wawo, magawo amumpingowo amene akufunikira anthu olalikira komanso kakhadi kosonyeza mapu a mbali ina ya gawolo. 2. M’bale wachinyamata akufotokozera mnzake mmene angagwiritsire ntchito mapu a gawo lawo.

DZIFUNSENI KUTI, ‘Kodi ndingathandize bwanji achinyamata amumpingo mwathu kuti azisangalala komanso azichita zambiri potumikira Yehova?’​—w18.03 11-12 ¶14-15.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena