Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb22 September tsamba 10
  • Tizidalira Yehova Kuti Atilimbikitse

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Tizidalira Yehova Kuti Atilimbikitse
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
  • Nkhani Yofanana
  • “Kodi Mukayikakayika Mpaka Liti?”
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
  • Zimene Tikuphunzira pa Nkhani ya Kulankhulana Bwino
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
  • B8 Kachisi Amene Solomo Anamanga
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
  • Kodi Mukukumbukira?
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2019
Onani Zambiri
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
mwb22 September tsamba 10

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Tizidalira Yehova Kuti Atilimbikitse

Eliya anachita mantha ndipo anathawa kuti apulumutse moyo wake (1Mf 19:3, 4; w19.06 15 ¶5)

Yehova anamuthandiza Eliya ndipo anamusonyeza mphamvu zake m’njira zodabwitsa kwambiri (1Mf 19:5-7, 11, 12; ia 103 ¶13; 106 ¶21)

Yehova anamupatsa ntchito yoti agwire (1Mf 19:15-18; ia 106 ¶22)

M’bale amene wamangidwa akulalikira kwa woyang’anira ndende.

Masiku ano, Yehova amatilankhula kudzera m’Mawu ake ndipo amatikumbutsa kuti amatikonda komanso kuti anatipatsa utumiki wofunika kwambiri woti tichite.​—1Ak 15:58; Akl 3:23.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena