Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb22 November tsamba 4
  • Yehova Anachita Zimene Anthu Sankayembekezera

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Yehova Anachita Zimene Anthu Sankayembekezera
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
  • Nkhani Yofanana
  • Mzimayi Woipa Komanso Wodzimva Analangidwa
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
  • Kuleza Mtima kwa Yehova Kuli ndi Malire
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
  • “Tili Ndi Ambiri Kuposa Amene Ali Ndi Iwowo”
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
  • Musamaiwale Kuti Muli mu Nthawi Yamapeto
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
Onani Zambiri
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
mwb22 November tsamba 4

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Yehova Anachita Zimene Anthu Sankayembekezera

Pa nthawi imene kunali njala yoopsa, Yehova anati tsiku lotsatira anthu adzakhala ndi chakudya chochuluka (2Mf 7:1; it-1 716-717)

Msilikali wa Isiraeli anakaikira zimene Yehova analonjeza (2Mf 7:2)

Yehova anachita zinthu zimene anthu sankayembekezera n’komwe kuti zingachitikedi (2Mf 7:6, 7, 16-18)

Banja la Mboni lili ku resitilanti ndipo likuonera nkhani pa TV zosonyeza atsogoleri a mayiko atakumana. Anthu onse omwe ali pamalopo akuonera nkhaniyo mwachidwi.

Yehova ananena kuti dzikoli lidzawonongedwa mwadzidzidzi komanso mosayembekezeka. (1At 5:2, 3) N’chifukwa chiyani tiyenera kukhulupirira mawu a Yehova?

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena