Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb23 January tsamba 3
  • Musamaiwale Kuti Muli mu Nthawi Yamapeto

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Musamaiwale Kuti Muli mu Nthawi Yamapeto
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
  • Nkhani Yofanana
  • Kuleza Mtima kwa Yehova Kuli ndi Malire
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
  • Yehova Anachita Zimene Anthu Sankayembekezera
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
  • N’chifukwa Chiyani Kudzichepetsa N’kwabwino?
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
  • “Nyamulani Mwana Wanu”
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
mwb23 January tsamba 3

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Musamaiwale Kuti Muli mu Nthawi Yamapeto

Yehova anachenjeza Ayuda kuti adzawakana akapitiriza kuchita zoipa (2Mf 24:2, 3; w01 2/15 12 ¶2)

Yehova anagwiritsa ntchito Ababulo kuti awononge Yerusalemu mu 607 B.C.E. (2Mf 25:8-10; w07 3/15 11 ¶10)

Yehova anapulumutsa anthu amene anamvera machenjezo ake (2Mf 25:11)

M’bale akulalikira mnzake wa kuntchito pa nthawi yopuma masana.

Kwa zaka zambiri, Yehova wakhala akuchenjeza anthu padziko lapansi kuti adzawononga “anthu osaopa Mulungu.”​—2Pe 3:7.

DZIFUNSENI KUTI, ‘Kodi ndimagwiritsa ntchito mpata uliwonse umene ndapeza kuti ndithandize ena kudziwa zimene Mulungu akutichenjeza?’​—2Ti 4:2.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena