Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb23 January tsamba 2
  • N’chifukwa Chiyani Kudzichepetsa N’kwabwino?

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • N’chifukwa Chiyani Kudzichepetsa N’kwabwino?
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
  • Nkhani Yofanana
  • Yosiya Anali ndi Anzake Abwino
    Phunzitsani Ana Anu
  • Kodi Tikuphunzira Chiyani Kuchokera pa Nyimbo Yotchedwa “Uta”?
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
  • Yosiya Anachita Zabwino
    Nsanja ya Olonda—2009
  • Yosiya Ankakonda Chilamulo cha Mulungu
    Zimene Tingaphunzire Munkhani za M’Baibulo
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
mwb23 January tsamba 2
Mfumu Yosiya akumvetsera modzichepetsa pamene mlembi wake Safani akuwerenga mpukutu.

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

N’chifukwa Chiyani Kudzichepetsa N’kwabwino?

Yosiya anali wofunitsitsa kusangalatsa Yehova (2Mf 22:1-5)

Iye anavomereza zolakwa za anthu ake modzichepetsa (2Mf 22:13; w00 9/15 29-30)

Chifukwa choti Yosiya anali wodzichepetsa, Yehova anamudalitsa (2Mf 22:18-20; w00 9/15 30 ¶2)

Yehova amasangalala nafe ngati modzichepetsa timamupempha kuti atitsogolere komanso timavomereza zomwe talakwitsa n’kukonza zolakwikazo.​—Yak 4:6.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena