Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb22 November tsamba 5
  • Anachita Zinthu Molimba Mtima, Modzipereka Komanso Mofunitsitsa

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Anachita Zinthu Molimba Mtima, Modzipereka Komanso Mofunitsitsa
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
  • Nkhani Yofanana
  • Yehu Anamenyera Nkhondo Kulambira Koyera
    Nsanja ya Olonda—2011
  • Yehova Anapereka Chilango kwa Mfumukazi Yoipa
    Zimene Tingaphunzire Munkhani za M’Baibulo
  • “Nyumba Yonse ya Ahabu Ifafanizidwe”​—2Mf 9:8
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
  • Muzifunsira Nzeru kwa Yehova
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
Onani Zambiri
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
mwb22 November tsamba 5
Yehu ali pa galeta lake ndipo akuuza nduna ya panyumba ya mfumu kuti iponyere Yezebeli panja kudzera pawindo.

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Anachita Zinthu Molimba Mtima, Modzipereka Komanso Mofunitsitsa

Yehova anatuma Yehu kuti akaphe anthu onse a m’nyumba ya Mfumu Ahabu yemwe anali woipa (2Mf 9:6, 7; w11 11/15 3 ¶2)

Yehu anachita zinthu mwamsanga popha Mfumu Yehoramu (mwana wa Ahabu) komanso Mfumukazi Yezebeli (yemwe anali mkazi wa Ahabu) (2Mf 9:22-24, 30-33; w11 11/15 4 ¶2-3; onani bokosi lakuti “‘Nyumba Yonse ya Ahabu Ifafanizidwe’​—2Mf 9:8”)

Yehu anachita zonse zimene Yehova anamuuza ndipo anasonyeza kuti anali wolimba mtima, wodzipereka komanso wofunitsitsa (2Mf 10:17; w11 11/15 5 ¶3-4)

DZIFUNSENI KUTI, ‘Kodi ndingatsanzire bwanji Yehu posonyeza kumvera lamulo lopezeka pa Mateyu 28:19, 20?’

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena