Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb22 November tsamba 16
  • Zimene Zingatithandize Kuti Tisamazengereze Pochita Zinthu

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Zimene Zingatithandize Kuti Tisamazengereze Pochita Zinthu
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
  • Nkhani Yofanana
  • Kuzengereza—Mbala ya Nthaŵi
    Galamukani!—1995
  • Ikapita Siibweranso Choncho Igwiritseni Ntchito Bwino
    Nsanja ya Olonda—2006
  • Kodi Ndingatani Kuti Ndisamachite Zinthu Mozengereza?
    Zimene Achinyamata Amafunsa
  • Anachita Zinthu Molimba Mtima, Modzipereka Komanso Mofunitsitsa
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
Onani Zambiri
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
mwb22 November tsamba 16
Zithunzi: 1. Yehu akudzozedwa pomuthira mafuta pamutu pake. 2. Yehu wakonzekera nkhondo ndipo akuyendetsa galeta.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

Zimene Zingatithandize Kuti Tisamazengereze Pochita Zinthu

Munthu wozengereza amasunthira patsogolo zinthu zimene amafunika kuchita panthawiyo. Zimenezi si zomwe Yehu anachita atapatsidwa utumiki ndi Yehova kuti akaphe anthu onse a m’nyumba ya Ahabu. (2Mf 9:6, 7, 16) Anthu ena amanena kuti: “Mwina ndibatizidwa zaka zikubwerazi.” “Ndiyamba kuwerenga Baibulo tsiku ndi tsiku posachedwapa.” “Ndidzayamba upainiya n’kadzapeza ntchito yabwino.” Malemba angatithandize kupewa kuzengereza tikamachita zinthu zokhudza kulambira.

Kodi malemba otsatirawa angatithandize bwanji kupewa kuchita zinthu mozengereza?

  • Mla 5:4

  • Mla 11:4

  • 1Ak 7:29-31

  • Yak 4:13, 14

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena