Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb23 May tsamba 8
  • Mukhoza Kutumikira Yehova Ngakhale Makolo Anu Si Chitsanzo Chabwino

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Mukhoza Kutumikira Yehova Ngakhale Makolo Anu Si Chitsanzo Chabwino
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
  • Nkhani Yofanana
  • Muzisonyeza Chikondi Chokhulupirika
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
  • Anatipatsa Ufulu Wosankha
    Nsanja ya Olonda—2010
  • “Anapitiriza Kumamatira Yehova”
    Nsanja ya Olonda—2012
  • Chitsanzo Chabwino—Hezekiya
    Mayankho a Zimene Achinyamata Amafunsa, Buku Lachiwiri
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
mwb23 May tsamba 8

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Mukhoza Kutumikira Yehova Ngakhale Makolo Anu Si Chitsanzo Chabwino

Mfumu Ahazi, yemwe anali bambo ake a Hezekiya, inachita zoipa zambiri (2Mb 28:1; w16.02 14 ¶8)

Hezekiya anasankha kutumikira Yehova ngakhale kuti bambo ake sanali chitsanzo chabwino (2Mb 29:1-3; w16.02 14 ¶9-11)

Hezekiya analimbikitsa ena kuti asasiye kutumikira Yehova chifukwa cha kusakhulupirika kwa bambo awo (2Mb 29:4-6)

Zithunzi: 1. M’bale wachinyamata akuwerenga magazini, pamene anthu ena a m’banja lake akukongoletsa nyumba yawo pokonzekera holide inayake. 2. M’bale yemwe uja akuyankha pa misonkhano ya mpingo.

DZIFUNSENI KUTI, ‘Kodi ndingalimbikitse bwanji achinyamata amene makolo awo satumikira Yehova?’

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena