Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb23 July tsamba 10
  • “Chimwemwe Chimene Yehova Amapereka Ndicho Malo Anu Achitetezo”

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • “Chimwemwe Chimene Yehova Amapereka Ndicho Malo Anu Achitetezo”
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
  • Nkhani Yofanana
  • Chimwemwe cha Yehova Ndicho Linga Lathu
    Nsanja ya Olonda—1995
  • Chimwemwe Chimene Yehova Amapereka
    Imbirani Yehova
  • Muzikhala Okhulupirika kwa Yehova Mukamasankha Anthu Ocheza Nawo
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
  • “Chimwemwe Chimene Yehova Amapereka”
    Imbirani Yehova Mosangalala
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
mwb23 July tsamba 10
Ezara wanyamula mpukutu ndipo akutamanda Yehova pamaso pa anthu.

Ezara akuwerengera anthu Chilamulo komanso akutamanda Yehova

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

“Chimwemwe Chimene Yehova Amapereka Ndicho Malo Anu Achitetezo”

Anthu anasonkhana kuti amvetsere pamene Ezara ankawerenga Chilamulo (Ne 8:1, 2; w13 10/15 21 ¶2; onani chithunzi chapachikuto)

Iyi inali nthawi yoti anthuwo asangalale ndi kulambira Yehova, osati yoti azilira chifukwa cha machimo omwe anachita m’mbuyo (Ne 8:9, 11, 12)

Chimwemwe chimene Yehova amapereka ndi malo achitetezo kwa atumiki ake (Ne 8:10; w07 7/15 22 ¶9-10)

Banja lachinyamata likucheza mosangalala ndi banja lachikulire pa msonkhano wa chigawo.

DZIFUNSENI KUTI, ‘Kodi ndili ndi zifukwa ziti zimene zingandipangitse kukhala wosangalala, ngakhale kuti ndikukumana ndi mavuto?’

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena