Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb23 September tsamba 6
  • Anagwiritsa Ntchito Udindo Wake Pothandiza Anthu Ena

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Anagwiritsa Ntchito Udindo Wake Pothandiza Anthu Ena
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
  • Nkhani Yofanana
  • Muzithandiza Ena Kuti Azichita Zambiri
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
  • Muzitsanzira Mmene Yehova Amagwiritsira Ntchito Udindo Wake
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
  • Kodi Chilamulo Chinkasonyeza Bwanji Kuti Yehova Amaganizira Anthu Osauka?
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
  • Mfundo Zothandiza Kuweruza Milandu Mwachilungamo
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
mwb23 September tsamba 6

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Anagwiritsa Ntchito Udindo Wake Pothandiza Anthu Ena

Moredekai anapatsidwa udindo waukulu kwambiri (Est 9:4; it-2 432 ¶2)

Iye anayambitsa chikondwerero cha chaka ndi chaka pofuna kulemekeza Yehova (Est 9:​20-22, 26-28; it-2 716 ¶5)

Iye ankachitira zabwino anthu a Mulungu (Est 10:3)

Mkulu wachinyamata wagwira pamkono mlongo wachikulire pamene ali limodzi mu utumiki.

Masiku ano, anthu amene ali ndi udindo m’gulu la Yehova amayesetsa kutsanzira chitsanzo cha Moredekai.—cl 101-102 ¶12-13.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena