CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
Muzitsanzira Mmene Yehova Amagwiritsira Ntchito Udindo Wake
Yehova ndi wolamulira wamkulu (1Mf 22:19; it-2 21)
Yehova amalemekeza amene amawalamulira (1Mf 22:20-22; w21.02 4 ¶9)
Yehova anadalitsa zomwe mngelo anachita (1Mf 22:23; it-2 245)
Akulu komanso mitu ya mabanja ayenera kutsanzira mmene Yehova amagwiritsira ntchito udindo. (Aef 6:4; 1Pe 3:7; 5:2, 3) Akamachita zimenezi anthu amene amawayang’anira amakhala osangalala.