Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb23 September tsamba 3
  • Muzithandiza Ena Kuti Azichita Zambiri

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Muzithandiza Ena Kuti Azichita Zambiri
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
  • Nkhani Yofanana
  • Anagwiritsa Ntchito Udindo Wake Pothandiza Anthu Ena
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
  • Zimene Tikuphunzira pa Nkhani ya Kulankhulana Bwino
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
  • Yesetsani Kukhala Odzichepetsa Ngati Esitere
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
  • Kodi Chilamulo Chinkasonyeza Bwanji Kuti Yehova Amaganizira Anthu Osauka?
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
mwb23 September tsamba 3

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Muzithandiza Ena Kuti Azichita Zambiri

Moredekai anapereka chitsanzo chabwino cha kukhala wolimba mtima komanso wokhulupirika kwa Yehova (Est 3:​2-4; it-2 431 ¶7)

Anathandiza Esitere kuona kuti akhoza kuchita zabwino (Est 4:​7, 8; it-2 431 ¶9)

Analimbikitsa Esitere kuti akhale wolimba mtima komanso azidalira Yehova (Est 4:​12-14; ia 133 ¶22-23)

Zithunzi: 1. Mkulu akulimbikitsa m’bale wachinyamata pamene ali mu utumiki. 2. M’bale wachinyamata uja akulemba fomu ya pa intaneti yofunsira Sukulu ya Akhristu Olalikira za Ufumu. 3. Kenako m’bale uja wamaliza maphunziro ake a sukulu ya SKE.

DZIFUNSENI KUTI, ‘Kodi zolankhula komanso zochita zanga zimathandiza ena mumpingo kuti azichita zambiri potumikira Yehova?’

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena