CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
Musamasiye Akhristu Anzanu
Abale ake a Yobu anasiya kuchita naye zinthu (Yob 19:13)
Anyamata ang’onoang’ono komanso antchito ake anasiya kumulemekeza (Yob 19:16, 18)
Anzake apamtima anamutembenukira (Yob 19:19)
DZIFUNSENI KUTI, ‘Kodi ndingatani kuti ndipitirize kusonyeza chikondi kwa Mkhristu mnzanga amene akukumana ndi mavuto?’—Miy 17:17; w22.01 16 ¶9; w21.09 30 ¶16; w90 9/1 22 ¶20.