Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • wp22 No. 1 tsamba 16
  • Anthu Akuvutika Ndi Chidani Padziko Lonse

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Anthu Akuvutika Ndi Chidani Padziko Lonse
  • Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yogawira)—2022
  • Nkhani Yofanana
  • N’zotheka Kuthetsa Chidani
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yogawira)—2022
  • N’chifukwa Chiyani Chidani Sichikutha?
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yogawira)—2022
  • N’chifukwa Chiyani Anthu Akudana Kwambiri?—Kodi Baibulo Limanena Zotani?
    Nkhani Zina
  • Nchifukwa Ninji Pali Chidani Chochuluka?
    Galamukani!—1997
Onani Zambiri
Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yogawira)—2022
wp22 No. 1 tsamba 16
Mwiniwake wasitolo waima pawindo lomwe lathyoledwa ndi akuba ndipo akuyang’ana panja. Antchito ake akutolera magalasi osweka.

Anthu Akuvutika Ndi Chidani Padziko Lonse

Anthu akuvutika kwambiri ndi chidani chomwe chili ponseponse padzikoli.

Nkhani zambiri zimene zikumafalitsidwa pa intaneti zikumasonyeza kuti anthu sakukondana. Mwachitsanzo, amatumizirana maimelo, makalata ngakhalenso mauthenga oipa osonyeza chidani. Taganiziraninso zinthu zambirimbiri zoipa zimene anthu amachitira ena monga kuwasala, kuwanyoza chifukwa cha mtundu wawo, kuwanenera mawu achipongwe, kuwaopseza komanso kuwawonongera zinthu zawo. Padzikoli anthu ambiri akusalidwa ndiponso kudedwa.

Magaziniyi ikufotokoza mmene chidani chingathere. Sikuti amenewa ndi maganizo ongolakalaka zinthu zabwino basi koma ndi zenizeni zomwe zayamba kale kuchitika padziko lonse lapansi.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena