Genesis 36:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pambuyo pake, Esau anatenga akazi ake, ana ake aamuna ndi aakazi komanso ena onse amʼnyumba yake, ziweto zake zonse ndi chuma chake chonse chimene anachipeza+ mʼdziko la Kanani nʼkupita kudziko lina, kutali ndi Yakobo mchimwene wake.+
6 Pambuyo pake, Esau anatenga akazi ake, ana ake aamuna ndi aakazi komanso ena onse amʼnyumba yake, ziweto zake zonse ndi chuma chake chonse chimene anachipeza+ mʼdziko la Kanani nʼkupita kudziko lina, kutali ndi Yakobo mchimwene wake.+