Genesis 36:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pambuyo pake, Esau anatenga akazi ake, ana ake aamuna ndi aakazi, ndi ena onse a m’nyumba yake, ziweto zake zonse ndi chuma chake+ chonse chimene anachipeza m’dziko la Kanani, n’kupita kudziko lina kutali ndi Yakobo m’bale wake.+
6 Pambuyo pake, Esau anatenga akazi ake, ana ake aamuna ndi aakazi, ndi ena onse a m’nyumba yake, ziweto zake zonse ndi chuma chake+ chonse chimene anachipeza m’dziko la Kanani, n’kupita kudziko lina kutali ndi Yakobo m’bale wake.+