Genesis 42:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Ndife ana a bambo mmodzi ndipo tinalipo ana aamuna 12.+ Koma mmodzi kulibenso,+ ndipo wamngʼono ali ndi bambo athu kudziko la Kanani.’+
32 Ndife ana a bambo mmodzi ndipo tinalipo ana aamuna 12.+ Koma mmodzi kulibenso,+ ndipo wamngʼono ali ndi bambo athu kudziko la Kanani.’+