Genesis 42:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Koma Rubeni anauza bambo ake kuti: “Ngati Benjamini sindidzabwera naye kwa inu, mudzaphe ana anga aamuna awiri.+ Mumupereke mʼmanja mwanga, ndipo ndidzamʼbwezera kwa inu.”+
37 Koma Rubeni anauza bambo ake kuti: “Ngati Benjamini sindidzabwera naye kwa inu, mudzaphe ana anga aamuna awiri.+ Mumupereke mʼmanja mwanga, ndipo ndidzamʼbwezera kwa inu.”+