Genesis 42:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Koma Rubeni anauza bambo ake kuti: “Ndikapanda kudzam’bwezera kwa inu Benjamini, mudzaphe ana anga awiri.+ Mum’pereke m’manja mwanga, ndipo ineyo ndi amene ndidzam’bwezere kwa inu.”+
37 Koma Rubeni anauza bambo ake kuti: “Ndikapanda kudzam’bwezera kwa inu Benjamini, mudzaphe ana anga awiri.+ Mum’pereke m’manja mwanga, ndipo ineyo ndi amene ndidzam’bwezere kwa inu.”+