Genesis 19:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Kenako Loti anachoka ku Zowari limodzi ndi ana ake aakazi awiri aja nʼkukakhala kudera lakumapiri,+ chifukwa ankachita mantha kukhala ku Zowari.+ Kumeneko, iye ndi ana ake awiriwo anayamba kukhala mʼphanga.
30 Kenako Loti anachoka ku Zowari limodzi ndi ana ake aakazi awiri aja nʼkukakhala kudera lakumapiri,+ chifukwa ankachita mantha kukhala ku Zowari.+ Kumeneko, iye ndi ana ake awiriwo anayamba kukhala mʼphanga.