Genesis 19:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Pambuyo pake Loti anachoka ku Zowari n’kukakhala kudera la kumapiri, iye limodzi ndi ana ake aakazi awiri aja,+ chifukwa anachita mantha kukhala ku Zowari.+ Kumeneko, iye ndi ana ake awiriwo anayamba kukhala m’phanga.
30 Pambuyo pake Loti anachoka ku Zowari n’kukakhala kudera la kumapiri, iye limodzi ndi ana ake aakazi awiri aja,+ chifukwa anachita mantha kukhala ku Zowari.+ Kumeneko, iye ndi ana ake awiriwo anayamba kukhala m’phanga.