Numeri 6:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Aziperekanso kwa Yehova nkhosa yamphongo monga nsembe yamgwirizano, limodzi ndi dengu la mikate yopanda zofufumitsa ija. Kenako wansembeyo azipereka nsembe yambewu+ ndi nsembe yachakumwa, zimene zimayendera limodzi ndi nsembe yamgwirizanoyo.
17 Aziperekanso kwa Yehova nkhosa yamphongo monga nsembe yamgwirizano, limodzi ndi dengu la mikate yopanda zofufumitsa ija. Kenako wansembeyo azipereka nsembe yambewu+ ndi nsembe yachakumwa, zimene zimayendera limodzi ndi nsembe yamgwirizanoyo.