88 Nyama zonse za nsembe yamgwirizano zinalipo ngʼombe 24 zamphongo, nkhosa 60 zamphongo, mbuzi 60 zamphongo ndi ana a nkhosa 60 amphongo, aliyense wosapitirira chaka chimodzi. Zimenezi ndi zimene anapereka pamwambo wotsegulira+ guwa lansembe, pambuyo poti ladzozedwa.+