Numeri 22:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Ndiyeno Balaki anafunsa Balamu kuti: “Kodi sindinatumize anthu kuti adzakuitaneni? Nanga nʼchifukwa chiyani simunabwere? Kodi mukuganiza kuti ineyo sindingathe kukupatsani mphoto yaikulu?”+
37 Ndiyeno Balaki anafunsa Balamu kuti: “Kodi sindinatumize anthu kuti adzakuitaneni? Nanga nʼchifukwa chiyani simunabwere? Kodi mukuganiza kuti ineyo sindingathe kukupatsani mphoto yaikulu?”+