Numeri 22:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Ndiyeno Balaki anafunsa Balamu kuti: “Kodi sindinatumize amithenga kuti adzakuitaneni? Nanga n’chifukwa chiyani simunabwere? Kodi mukuganiza kuti ineyo sindingathe kukupatsani ulemerero wochuluka?”+
37 Ndiyeno Balaki anafunsa Balamu kuti: “Kodi sindinatumize amithenga kuti adzakuitaneni? Nanga n’chifukwa chiyani simunabwere? Kodi mukuganiza kuti ineyo sindingathe kukupatsani ulemerero wochuluka?”+