Numeri 36:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iwo anati: “Paja Yehova anakulamulani inu mbuyathu, kuti mugawe dzikoli pochita maere+ kuti likhale cholowa cha Aisiraeli. Yehova anakulamulaninso kuti mupereke cholowa cha mchimwene wathu Tselofekadi kwa ana ake aakazi.+
2 Iwo anati: “Paja Yehova anakulamulani inu mbuyathu, kuti mugawe dzikoli pochita maere+ kuti likhale cholowa cha Aisiraeli. Yehova anakulamulaninso kuti mupereke cholowa cha mchimwene wathu Tselofekadi kwa ana ake aakazi.+